Mundiyalikira gome pamaso panga m'kuona kwa adani anga:Mwandidzoza mutu wanga mafuta; cikho canga cisefuka.