Ambuye wapepula ngwazi zanga zonse pakati panga;Waitanira msonkhano pa ine kuti uphwanye anyamata anga,Ambuye wapondereza namwaliyo, mwana wamkazi wa Ziyoni, monga mopondera mphesa.