Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 9:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo anati kwa Aroni, Dzitengere mwana wa ng'ombe wamwamuna, akhale nsembe yaucimo, ndi nkhosa yamphongo ikhale nsembe yopsereza, zopanda cirema, nubwere nazo pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 9

Onani Levitiko 9:2 nkhani