Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 8:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anatengako mafuta odzoza, ndi mwazi unakhala pa guwa la nsembewo, naziwaza pa Aroni, pa zobvala zace, ndi pa ana ace amuna, ndi pa zobvala za ana ace amuna omwe; napatula Aroni, ndi zobvala zace, ndi ana ace amuna, ndi zobvala za ana ace amuna omwe.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 8

Onani Levitiko 8:30 nkhani