Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 8:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anatenga ngangayo naiweyula, nsembe yoweyula pamaso pa Yehova; ndilo gawo la Mose la ku nkhosa yamphongo ya kudzaza manja; monga Yehova adamuuza Mose.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 8

Onani Levitiko 8:29 nkhani