Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 8:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Mose anazicotsa ku manja ao, nazitentha pa guwa la nsembe, pa nsembe yopsereza; ndizo nsembe zodzaza manja zocita pfungo lokoma; ndiyo nsembe yamoto ya kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 8

Onani Levitiko 8:28 nkhani