Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 6:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wansembe abvale mwinjiro wace wabafuta, nabvale pathupi pace zobvala za pamiyendo zabafuta; naole phulusa, mota utanyeketsa nsembe yamoto pa guwa la nsembe, nalitaye m'mphepete mwa guwa la nsembe.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 6

Onani Levitiko 6:10 nkhani