Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 6:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uza Aroni ndi ana ace, ndi kuti, Cilamulo ca nsembe yopsereza ndi ici: nsembe yopsereza izikhala pa nkhuni za pa guwa la nsembe usiku wonse kufikira m'mawa; ndipo mota wa pa guwa la nsembe uziyakabe pamenepo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 6

Onani Levitiko 6:9 nkhani