Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adze naco kwa wansembe, ndi wansembeyo atengeko wodzala manja ukhale cikumbutso cace, nacitenthe pa guwa la nsembe monga umo amacitira nsembe zamoto za Yehova; ndiyo nsembe yaucimo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 5

Onani Levitiko 5:12 nkhani