Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 5:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma cuma cace cikapanda kufikira njiwa ziwiri kapena maunda awiri, wocimwayo azidza naco copereka cace limodzi la magawo khumi la efa la ufa wosalala, likhale la nsembe yaucima; asamaikapo mafuta, kapena kuikapo libona ai; pakuti ndico nsembe yaucimo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 5

Onani Levitiko 5:11 nkhani