Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 5:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wansembe amcitire comtetezera cifukwa ca kucimwa kwace adacimwira cimodzi ca izi, ndipo adzakhululukidwa; ndipo cotsalira cikhale ca wansembe, monga umo amacitira copereka caufaco.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 5

Onani Levitiko 5:13 nkhani