Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 24:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwana wamwamuna wa mkazi M-israyeli, atate wace ndiye M-aigupto, anaturuka mwa ana a Israyeli; ndi mwana wamwamuna wa mkazi M-israyeliyo analimbana naye munthu M-israyeli kucigono;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 24

Onani Levitiko 24:10 nkhani