Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 24:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ukhale wa Aroni ndi ana ace, audye pamalo popatulika; pakuti auyese wopatulikitsa wocokera ku nsembe zamoto za Yehova; ndilo lemba losatha.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 24

Onani Levitiko 24:9 nkhani