Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 24:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo mwana wamwamuna wa mkazi M-israyeli anacitira DZINA mwano, natemberera; ndipo anadza naye kwa Mose. Dzina la mai wace ndiye Selomiti, mwana wa Dibri, wa pfuko la Dani.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 24

Onani Levitiko 24:11 nkhani