Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 16:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ici cikhale kwa inu lemba losatha, kucita cotetezera ana a Israyeli, cifukwa ca zocimwa zao zonse, kamodzi caka cimodzi. Ndipo anacita monga Yehova adauza Mose.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:34 nkhani