Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 16:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo acite cotetezera malo opatulikatu, natetezere cihema cokomanako, ndi guwa la nsembe; momwemo atetezerenso ansembe, ndi anthu onse a msonkhanowo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:33 nkhani