Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 13:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wansembe akaona nthenda yamfundu, ndipo taonani, ioneka yosakumba kubzola khungu, ndipo palibe tsitsi lakuda pamenepo, wansembe ambindikiritse iye ali ndi mfundu masiku asanu ndi awiri;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:31 nkhani