Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 13:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

wansembe aziona nthenda; ndipo taonani, ngati ioneka yokumba kubzola khungu, ndipo pali tsitsi loyezuka lotetemera; pamenepo wansembe amuche wodetsedwa; ndiyo mfundu, ndilo khate la mutu kapena ndebvu.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:30 nkhani