Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 1:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Lankhula ndi ana a lsrayeli, nunene nao, Ali yense mwa inu akabwera naco copereka ca kwa Yehova, muzibwera naco copereka canu cikhale ca zoweta, ca ng'ombe, kapena ca nkhosa, kapena ca mbuzi.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 1

Onani Levitiko 1:2 nkhani