Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Copereka cace cikakhala nsembe yopsereza ya ng'ombe, azibwera nayo yaimuna yopanda cirema; abwere nayo ku khomo la cihema cokomanako, kuti alandirike pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 1

Onani Levitiko 1:3 nkhani