Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 1:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo copereka cace ca kwa Yehova cikakhala nsembe yopsereza ya mbalame, azibwera naco copereka cace cikhale ca njiwa, kapena ca maunda.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 1

Onani Levitiko 1:14 nkhani