Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma atsuke ndi madzi matumbo ndi miyendo; ndi wansembe abwere nazo zonse nazitenthe pa guwa la nsembe; ndiyo nsembe yopsereza, nsembe yamoto, ya pfungo lokoma la kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 1

Onani Levitiko 1:13 nkhani