Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 9:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sadzatsanulira Yehova nsembe zavinyo; sizidzamkomera Iye nsembe zao; zidzakhala kwa iwo ngati mkate wa acisoni; onse akudyako adzadetsedwa; pakuti mkate wao udzakhala wa njala yao, uwu sudzalowa m'nyumbaya Yehova.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 9

Onani Hoseya 9:4 nkhani