Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 48:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Israyeli anatambalitsa dzanja lace lamanja, naliika pa mutu wa Efraimu, amene ndiye wamng'ono, ndi dzanja lace lamanzere pa mutu wa Manase anapingasitsa manja ace dala; cifukwa Manase anali woyamba.

Werengani mutu wathunthu Genesis 48

Onani Genesis 48:14 nkhani