Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 48:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anatenga iwo onse awiri, Efraimu m'dzanja lace lamanja ku dzanja lamanzere la Yakobo, ndi Manase m'dzanja lace lamanzere ku dzanja lamanja la Israyeli, nadza nao pafupi ndi iye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 48

Onani Genesis 48:13 nkhani