Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 48:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadalitsa Yosefe, nati, Mulungu, pamaso pace anayenda makolo anga Abrahamu ndi Isake, Mulungu amene anandidyetsa ine nthawi zonse za moyo wanga kufikira lero,

Werengani mutu wathunthu Genesis 48

Onani Genesis 48:15 nkhani