Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 47:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati, Undilumbirire ine; namlumbirira iye. Ndipo Israyeli anawerama kumutu kwa kama.

Werengani mutu wathunthu Genesis 47

Onani Genesis 47:31 nkhani