Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 47:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

tiferenji pamaso panu, ife ndi dziko lathu? mutigule ife ndi dziko lathu ndi cakudya, ndipo ife ndi dziko lathu tidzakhala akapolo a Farao; ndipo mutipatse ife mbeu, kuti tikhale ndi moyo, tisafe, ndi kuti dziko lisakhale labwinja.

Werengani mutu wathunthu Genesis 47

Onani Genesis 47:19 nkhani