Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 47:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Citatha caka cimeneco, anadza kwa iye caka caciwiri, nati kwa iye, Sitibisira mbuyathu kuti ndalama zathu zonse zatha; ndipo zoweta za ng'ombe oza mbuyathu: palibe kanthu kotsala pamaso pa mbuyathu, koma matupi athu ndi maiko athu;

Werengani mutu wathunthu Genesis 47

Onani Genesis 47:18 nkhani