Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 47:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza nazo ng'ombe zao kwa Yosefe, ndipo Yosefe anapatsa iwo cakudya cosinthana ndi akavalo, ndi nkhosa, ndi ng'ombe, ndi aburu; ndipo anawadyetsa iwo ndi cakudya cosinthana ndi zoweta zao zonse caka cimeneco.

Werengani mutu wathunthu Genesis 47

Onani Genesis 47:17 nkhani