Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 39:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anasiya zace zonse m'manja a Yosefe; osadziwa comwe anali naco, koma cakudya cimene anadya. Ndipo Yosefe anali wokoma thupi ndi wokongola.

Werengani mutu wathunthu Genesis 39

Onani Genesis 39:6 nkhani