Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 39:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali ciyambire anamuyesa iye woyang'anira pa nyumba yace, ndi pa zace zonse, Yehova anadalitsa nyumba ya M-aigupto cifukwa ca Yosefe; ndipo mdalitso wa Yehova unali pa zace zonse, m'nyumba ndi m'munda.

Werengani mutu wathunthu Genesis 39

Onani Genesis 39:5 nkhani