Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 38:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atacuruka masiku mwana wamkazi wa Sua, mkazi wace wa Yuda anafa; ndipo Yuda anatonthola mtima, nakwera kunka kwa akusenga nkhosa zace ku Timna, iye ndi bwenzi lace Hira, M-adulami.

Werengani mutu wathunthu Genesis 38

Onani Genesis 38:12 nkhani