Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 38:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yuda anati kwa Tamara mpengozi wace, Khala wamasiye m'nyumba ya atate wako, kufikira akakula msinkhu Sela mwana wanga wamwamuna; cifukwa anati kuti, Angafe iyenso monga abale ace. Ndipo Tamara ananka nakhala m'nyumba ya atate wace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 38

Onani Genesis 38:11 nkhani