Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 30:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzapita ine lero pakati pa ziweto zonse ndi kusankhasankha m'menemo zoweta zonse zamathotho-mathotho ndi zamaanga-maanga, ndi za nkhosa zonse, ndi mbuzi zonse zamaangamaanga ndi zamathotho-mathotho: zotero zidzakhala malipiro anga.

Werengani mutu wathunthu Genesis 30

Onani Genesis 30:32 nkhani