Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 30:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cotero cilungamo canga cidzandibvomereza m'tsogolomo, pamene udzandifika cifukwa ca malipiro amene ali patsogolo pako; iri yonse yosakhala yamathotho-mathotho ndi yamaanga-maanga ya mbuzi, ndi iri yonse ya mbuzi yosakhala yakuda, ikapezedwa ndi ine, udzaiyesa yakuba.

Werengani mutu wathunthu Genesis 30

Onani Genesis 30:33 nkhani