Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 30:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Rakele anati, Taonani mdzakazi wanga Biliha, mulowe kwa iye; ndipo iye adzabala pa maondo anga, kuti inenso ndionerepo ana pa iye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 30

Onani Genesis 30:3 nkhani