Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 30:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anapsa mtima ndi Rakele; nati, Kodi ine ndikhala m'malo a Mulungu amene akukaniza iwe zipatso za mimba?

Werengani mutu wathunthu Genesis 30

Onani Genesis 30:2 nkhani