Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 28:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, Ine ndiri pamodzi ndi iwe, ndipo ndidzakusunga iwe konse kumene upitako, ndipo ndidzakubwezanso iwe ku dziko lino; cifukwa kuti sindidzakusiya iwe, kufikira kuti nditacita cimene ndanena nawe.

Werengani mutu wathunthu Genesis 28

Onani Genesis 28:15 nkhani