Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 28:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anauka m'tulo tace, nati, Ndithu, Yehova ali mommuno; ndipo sindinadziwe.

Werengani mutu wathunthu Genesis 28

Onani Genesis 28:16 nkhani