Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 27:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Esau anamuda Yakobo cifukwa ca mdalitso umene atate wace anamdalitsa nao: ndipo Esau anati m'mtima mwace, Masiku a maliro a atate wanga ayandikira; pamenepo ndipo ndidzamupha mphwanga Yakobo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 27

Onani Genesis 27:41 nkhani