Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 24:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mnyamatayo anaika dzanja lace pansi pa ncafu yace ya Abrahamu mbuye wace, namlumbirira iye za cinthuco.

Werengani mutu wathunthu Genesis 24

Onani Genesis 24:9 nkhani