Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 24:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mnyamatayo anatenga ngamila khumi za mbuyace, namuka: cifukwa kuti cuma conse ca mbuyace cinali m'dzanja lace: ndipo anacoka namuka ku Mesopotamiya, ku mudzi wa Nahori.

Werengani mutu wathunthu Genesis 24

Onani Genesis 24:10 nkhani