Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 24:53 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mnyamatayo anaturutsa zokometsera zasiliva ndi zokometsera zagolidi, ndi zobvala, nampatsa Rebeka: ndipo anapatsa za mtengo wapatari kwa mlongo wace ndi amace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 24

Onani Genesis 24:53 nkhani