Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 24:54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadya namwa iye ndi anthu amene anali pamodzi naye, nagonapo usiku: ndipo anauka m'mamawa, ndipo iye anati, Mundilole ine ndinke kwa mbuyanga.

Werengani mutu wathunthu Genesis 24

Onani Genesis 24:54 nkhani