Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 24:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinamfunsa iye kuti, Ndiwe mwana wa yani kodi? Ndipo anati, Ndine mwana wa Betuele, mwana wa Nahori amene anambalira iye Milika: ndipo ndinaika mphete pamphuno pace ndi zingwinjiri pa manja ace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 24

Onani Genesis 24:47 nkhani