Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 24:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinawerama mutu wanga ndi kulambira Yehova, ndi kumyamikira Yehova, Mulungu wa mbuyanga Abrahamu, amene ananditsogolera ine m'njira yakuona, kuti ndikamtengere mwana wamwamuna wace mwana wamkazi wa mphwace wa mbuyanga.

Werengani mutu wathunthu Genesis 24

Onani Genesis 24:48 nkhani