Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 24:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anafulumira, natsitsa mtsuko pa phewa lace, nati, Imwatu, ndipo ndidzamwetsanso ngamila zako: ndipo ndinamwa, ndipo anamwetsa ngamila.

Werengani mutu wathunthu Genesis 24

Onani Genesis 24:46 nkhani