Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 19:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati iwo, Baima; natinso, Uyu anadza kuno kukhala ngati mlendo, ndipo afuna kutilamulira; tsopano tidzakucitira iwe koipa koposa iwo. Ndipo iwo anamkakamiza munthuyo Loti ndithu, nayandikira kuti aswe citseko.

Werengani mutu wathunthu Genesis 19

Onani Genesis 19:9 nkhani