Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 19:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonanitu, ndiri ndi ana akazi awiri, amene sanadziwe mwamuna; ndiwaturutsire iwo kwa inu, mucite nao comwe cikomera inu; koma anthu awa musawacitire iwo kanthu; cifukwa kuti anadza iwo pansi pa mthunzi wa cindwi langa,

Werengani mutu wathunthu Genesis 19

Onani Genesis 19:8 nkhani